Yesu anatcha Msamariyayo “mnansi wabwino”
pamene adayika mtima wake wonse kupulumutsa munthu akufa,
ndipo Yesu anatipempha kuti “tichitenso chimodzimodzi.
Ziwalo za Mpingo wa Mulungu ndi zobadwanso
ngati anthu abwino amene amapulumutsa miyoyo,
polalikira mawu amoyo ku dziko lonse lapansi,
kotero kuti miyoyo yambiri ibwererenso m'manja
a Khristu Ahnsahnghong ndi Amayi Akumwamba.
“Kodi ukuganiza Ndi ndani mwa atatuwa, amene anali mnansi wa munthu amene anavulazidwa ndi achifwambawo?” . . . Yesu anamuwuza kuti, “Pita, uzikachita chimodzimodzi.” Luka 10:36–37
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi