Chifukwa chomwe aneneri amapemphaa anthu kuti asayiwale kuti padzakhala tsiku chiweruziro ndi chifukwa chakuti moyo wa munthu aliyense payekha komanso moyo wawo wachikhulupiriro zimalembedwa m inbuku la Mulungu. Mulungu adzaweruza munthu aliyense malinga ndi zonse zomwe anachita monga zalembedwera m inbuku.
Christ Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi anabwera kudziko lapansi kudzapereka chowonadi cha Pangano Latsopano kwa anthu omwe anachimwa Kumwamba. Anachita izi kuti anthu onse athe kulandira chikhululukiro cha machimo ndikubwerera Kumwamba patsiku chiweruziro.
Zochimwa za anthu ena zili zooneka kale zitsogola kunka kumlandu; koma enanso ziwatsata.Momwemons, pali ntchito zokoma zinaonekera kale; ndipo zina zosati zotere sizikhoza kubisika.
1 Timoteo 5: 24-25
Ndipo popeza kwaikikatu kwa anthu kufa kamodzi, ndipo atafa chiweruziro…
Ahebri 9:27
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi