Pamene sitinamvetse bwino chifuniro cha Mulungu ndi choonadi, tinkalankhula ngati
kamwana, kuganiza ngati kamwana, ndi kulingalira ngati kamwana, ndi kufuna kuti zonse zichitike
mogwirizana ndi zokhumba zathu. Komabe, titakhulupilira Kudza Kwachiwiri kwa Khristu
Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi ndi kuzindikira chowonadi, tiyenera kubadwanso monga ana a
Mulungu ndi chikhulupiriro chokhwima ndi kutsatira chitsogozo cha Mulungu momvera.
Monga momwe mapiri onse, mitsinje, ndi nyanja, zomwe zimapanga chilengedwe, zimakhutira ndi malo
awo osankhidwa ndikutsatira momvera chifuniro cha Mulungu m’malo awo opatsidwa popanda kudandaula, mamembala a Mpingo wa Mulungu amayenda njira
ya chikhulupiriro, nthawi zonse kufotokoza kuyamika m’malo awo opatsidwa.
Pamene ndinali mwana, ndinalankhula ngati mwana,
ndinalingirira ngati mwana, ndinawerenga ngati mwana;
tsopano ndakhala munthu, ndayesa chabe zachibwana.
1 Akorinto 13:11
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi