Kudzera mu ziphunzitso za m’Baibulo, Atate Akumwamba Ahnsahnghong ndi Amayi Akumwamba
anatiuza kuti tiyenera kuganizira za chifunilo cha Mulungu poyamba, osataya mtima koma kukhala othokoza pamavuto aliwonse, monga Yoswa ndi Kalebe.
Ana a Mulungu ayenera nthawi zonse kuganizira chiyankhulo cha Kumwamba.
Kutsatira ziphunzitso za Amayi, nthawi zonse tiyenera kugwiritsa ntchito mawu othokoza komanso kulimbikitsana, ndi kusamala osanena chirichonse cholakwika ndi maganizo akanthawi monga Mose anachitira.
“. . . munthu adzazengedwa mlandu chifukwa cha mawu aliwonse wopanda pake amene anayankhula. Pakuti ndi mawu anu mudzapezeka osalakwa ndiponso ndi mawu anu mudzapezeka olakwa.” Mateyu 12:36–37
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi