Nsomba zamoyo zimathetsa mavuto ndikusambira kumtunda. Momwemonso, tiyenera kupeza chifukwa choyamikira ngakhale m’malo ovuta, ndikupatsa Mulungu ulemerero potilola kupita ku Ufumu Wakumwamba komwe kulibe zowawa.
Khristu Ahnsahnghong wabwera kudziko losautsali kuti aphunzitse anthu njira yolandila chikhululukiro cha machimo ndi moyo wosatha ndikupita Kumwamba. Tiyenera kuzindikira chisomo cha Khristu Ahnsahnghong ndi
Mulungu Amayi, ndikugonjetsa masautso athu ndi zovuta zathu ndikuthokoza.
Onetsetsani kuti wina asabwezere choyipa kwa omuchitira choyipa koma nthawi zonse yesetsani kukhala okoma mtima kwawina ndi mnzake; ndiponso ndi kwa anthu ena onse. Kondwerani nthawi zonse, Pempherani kosalekeza, Yamikani mu zones. . . . 1 Atesalonika 5:15–18
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi