Baibulo limaneneratu kuti opatulika a Mulungu
ali ngati Isake—woloŵa m’malo wa Abrahamu
ndi iwo okhala mu Ziyoni adzakhala
achimwemwe ndi chisangalaro.
Kupyolera m’maulosi ameneŵa, tikutha kuona kuti
Mulungu amafuna kuti ana a Ziyoni
akhale osangalala nthaŵi zonse, monga momwe
tanthauzo la dzina la Isake limatanthauza[kuseka].
Pachifukwa ichi, akhristu a mpingo wa
Mulungu, omwe ali ndi chiyembekezo chopita
kumwamba ndikukhala moyo wogawana chikondi cha
Mulungu, amadzazidwa ndi chiyamiko ndi kuseka.
Monga momwe kuli katswiri wa zomangamanga
pomanga nyumba, palinso Katswiri Wopanga
moyo wosatha umene anthu onse amaulakalaka.
Popeza kuti palibe wina aliyense kupatulapo
Mulungu amene ali ndi moyo wosatha
m’chilengedwe chonse, Atate Kristu Ahnsahnghong ndi
Mulungu Amayi anabwera ku dziko lapansi
lino kudzapatsa anthu moyo wosatha.
Ndipo Mulungu anati, Koma Sara mkazi
wako adzakubalira iwe mwana wamwamuna;
ndipo udzamutcha dzina lake Isaki; [kuseka].
Genesesi 17:19
Koma ife, abale, monga Isaki,
tili ana a lonjezano.
Agalatiya 4:28
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi