Malinga ndi ulosi wa Yesaya 60, dzikoli lili mumdima.
Choncho, timakumana ndi zovuta zambiri m’moyo wathu.
Ngakhale kuti malo ndi
amudima komanso osasangalatsa,
mamembala a Mpingo wa
Mulungu amayesetsa kukhala kuunika
kwa dziko kudzera mu
ntchito zabwino ndi kupereka
chikondi cha Mulungu ku
dziko lopanda chikondili pomvera
mawu a Mulungu Amayi
akuti, “Khalani nyali yowala.
amaunikira mdima.”
Inu ndinu kuunika kwa
dziko lapansi. . . . Chomwecho
muwalitse inu kuunika kwanu
pamaso pa anthu, kuti
pakuona ntchito zanu zabwino,
alemekeze Atate wanu
wa Kumwamba.
(Mateyu 5:14-16)
Dziko losamvesetseka limene aliyense
amalota ndi ufumu wakumwamba.
Ana a kuunika ayenera kukwaniritsa
udindo wawo kuunikira mdima
pa kulalikira uthenga wabwino
wa ufumu wakumwamba, dziko
la maloto, kwa anthu
onse amene ali mumdima.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi