Mulungu anakhazikitsa pangano la chikondi, Pangano Latsopano,
kufikira pokhetsa mwazi pa mtanda
chifukwa cha machimo aanthu,
kupirira kunyozedwa ndi m’nyozo wochokera ku zolengedwa Zake zomwe.
Mulungu adabwera padziko lapansi monga dipo kuti atiwombole
kuti momwe Mulungu amatikondera,
ifenso tithe kukondana wina ndi mnzake ndi kufika pakulapa koona mtima.
Mulungu, yemwe adabweranso padziko lapansi pano
monga dipo lopulumutsa anthu,
ndi Khristu Ahnsahnghong ndi Amayi A Kumwamba
mu Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu.
. . . Monga Mwana wa Munthu sanadze kutumikiridwa koma kutumikira, ndi kupereka moyo wake dipo la anthu ambiri. Mateyu 20:28
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi