Ana a Mulungu anayesedwa ndi nthanda ya Kumwamba ndipo anaponyedwa padziko lapansi. Kutsogolera wochimwa wina kulapa kupyolera mu ulaliki ndi mchitidwe wokongola wa kulapa machimo athu ndi kubwerera kumudzi wathu kumwamba. Izi ndi zomwe Mulungu amakondwera nazo.
Mpingo wa World Mission Society Church of God ndi mpingo wokhawo padziko lapansi umene umafalitsa chikondi cha Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi amene abwera padziko lapansi kudzapulumutsa ochimwa. Ndiponso, ndi mpingo wokhawo umene umasunga Tsiku la Sabata ndi Paskha umene Mulungu analamula anthu ake kusunga, ndi kuphunzitsa malamulo onsewa kwa anthu.
Ndidzafika kwa Yehova ndi chinai, ndi kuwerama kwa Mulungu Wam’mwamba? Kodi ndifike kwa Iye ndi nsembe zopsereza, ndi anaang’ombe a chaka chimodzi? Kodi Yehova adzakondwera nazo nkhosa zamphongo zikwi, kapena ndi mitsinje ya mafuta zikwi khumi? Kodi ndipereke mwana wanga woyamba chifukwa cha kulakwa kwanga, chipatso cha thupi langa chifukwa cha kuchimwa kwa moyo wanga?
Mika 6:6–8
Ndinena kwa inu, kotero kudzakhala chimwemwe Kumwamba chifukwa cha wochimwa mmodzi wotembenuka mtima, koposa anthu olungama makumi asanu ndi anai mphambu asanu ndi anai, amene alibe kusowa kutembenuka mtima.
Luka 15:7
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi