M’nthawi ya Chipangano Chakale, machimo onse omwe anthu adachita
m’chaka chatha adasamutsidwira kumalo opatulika
ndipo pa Tsiku la Chitetezero, mbuzi ya Azazele
imatenga machimowo napita nawo kumalo kayokha m’chipululu, n’kufera konko;
n’kuthetseratu tchimo.
Tsiku la Chitetezero ndi phwando lomwe limatidziwitsa za nsembe
ya Atate ndi Amayi a Kumwamba, omwe adakhala nsembe zamachimo.
Popanga Satana, amene adatichimwitsa, kulipira machimo onse,
Amatitetezera machimo ife.
Koma kunakomera Yehova kumtundudza; anammvetsa zowawa; moyo wake ukapereka nsembe yopalamula, Iye adzaona mbeu yake . . . Yesaya 53:10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi