Phwando la masiku khumi (10) lomwe liyamba pa Phwando la Malipenga
mpaka pa Tsiku la Chitetezero ndi nthawi yofunika kulapa yomwe
Mulungu amapereka kwa anthu.
Baibulo limatitsegula maso n’kutidzutsa kuzamoyo wathu wakale
kudzera pa nkhani ya Mfumu ya ku Babulo ndi ya Mfumu ya Tiro.
Khristu Ahnsahnghong ndi Amayi A Kumwamba adabwera padziko lapansi
ndi Pangano Latsopano, njira yachipulumutso,
kuti anthu onse alape ndi mtima wonse.
Mamembala a Mpingo wa Mulungu akuyesetsa
kumvera mawu a Mulungu ndi kusachitanso machimo,
pokhala moyo wolapa.
nanena, Nthawi yakwanira, ndipo Ufumu wa Mulungu wayandikira; tembenukani mtima, khulupirirani Uthenga Wabwino!. Marko 1:15
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi