Zinthu zimene zimakondweretsa Mulungu
zinalembedwa m’mabuku a Luka, Aheberi,
Yeremiya ndi Miyambo. Ndiwo kulapa kwa wochimwa,
chikhulupiriro chowona mtima, kudzitamandira ndi za
Mulungu, ndi awo amene njira zawo ziri zangwiro.
Mulungu anatiphunzitsa kuti zonsezi zikhoza kutheka
ndi ntchito yolalikira imene imatsogolera anthu
ambiri kuti adzapulumuke.
Ana pa dziko lapansi pano amapatsa makolo awo
mphatso zimene zimakondweretsa makolo awo ndi
mtima wonse. Momwemonso, ana akumwamba
amachita zomwe zimakondweretsa Atate
wakumwamba Christ Ahnsahnghong ndi Mulungu
Amayi koposa. Monga momwe Yesu
analamulira zaka 2,000 zapitazo, iwo
amapereka mitima yawo kuti apeze
ma membala a banja lotayika lakumwamba.
[P]akuti kale munali mdima, koma
tsopano muli kuunika mwa Ambuye;
yendani monga ana a kuunika, pakuti
chipatso cha kuunika tichipeza mu
ubwino wonse, ndi chilungamo, ndi
choonadi, kuyesera chokondweretsa
Ambuye nchiyani.
Aefeso 5:8-10
[A]mene afuna anthu onse apulumuke,
nafike pozindikira choonadi.
1 Timoteyo 2:4
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi