Mulungu sanabweretse masoka amene anafuna kubweretsa
ku Nineve chifukwa iwo analapa moona
mtima ngakhale kuti anatsatira milungu ina
ndi kuzunza Aisiraeli.
Pamene wachifwamba wa kumanja ndi mwana
woloŵerera amene anasiya atate wake analapa,
iwo analandira madalitso.
Kupyolera mu zonsezi, Mulungu anasonyeza anthu
kuti angathe kupeŵa masoka ndi kupulumutsidwa
akalapa machimo awo.
Kuuma mtima ndi mtima wosalapa umasunga
mkwiyo wa Mulungu pa Tsiku la Chiweruzo.
Mamembala a Mpingo wa Mulungu anafika
podziŵa njira ya kulapa kotheratu kudzera
m’mawu a Kristu Ahnsahnghong ndi Mulungu
Amayi, ndipo tsopano akulalikira uthenga wa
pangano latsopano, ndi chiyembekezo chakuti enanso
adzapulumutsidwa mwa kulapa.
Chifukwa chake ndidzakuweruzani inu, nyumba ya
Israele, yense monga mwa njira zake,
ati Ambuye Yehova. Bwererani, nimutembenukire kuleka
zolakwa zanu zonse, ndipo simudzakhumudwa nazo,
ndi kuonongeka nayo mphulupulu.
Ezekieli 18:30
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi