Mulungu analola Aisrayeli kuwomba lipenga la kulapa pa Phwando la Malipenga, tsiku loyamba la mwezi wachisanu ndi chiwiri pa kalendala yopatulika kuti akonzekere Tsiku la Chitetezero, tsiku lakhumi la mwezi wachisanu ndi chiwiri malingana ndi kalendala yopatulika pamene Mose analandira. Malamulo Khumi kachiwiri.
Kuuzimu, ndi phwando limene likulimbikitsa anthu onse, amene anachita machimo osakhululukidwa kumwamba ndipo anathamangitsidwa padziko lapansi pano, kuti alape, nati, “Lapani kudzera mu pangano latsopano ndi kubwerera kwa Mulungu.”
Lero, pamene Ufumu wa Kumwamba ukayandikira, iwo amene analonjezedwa ufumu wakumwamba pa kulapa kotheratu ayenera kuliza lipenga la nsembe ndi chikondi cha Mulungu amene anawapulumutsa kudzera mu pangano latsopano kuti dziko lonse lilape ndi kubwerera kwa Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
“Nena ndi ana a Israele, ndi kuti, ‘Mwezi wachisanu ndi chiwiri, tsiku loyamba la mweziwo, muzipumula, ndiko chikumbutso cha kuliza malipenga, msonkhano wopatulika.’ ”
Levitiko 23:24
nanena, “Nthawi yakwanira,” “ndipo Ufumu wa Mulungu wayandikira; tembenukani mtima, khulupirirani Uthenga Wabwino.”
Marko 1:15
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi