Kale, pamene Aisraele adachimwa, adalipira machimo awo ndi mwazi wa nyama m’malo opatulika. Machimo omwe anthu amasunga malo yopatulika chaka chonse adabwezedwa ku Azazeli, yemwe amayimira Satana, ndi wansembe wamkulu pa Tsiku la Chitetezo, tsiku lakhumi la mwezi wachisanu ndi chiwiri pakalendala yopatulika. Ntchitoyi ikuchitika kudzera mu Tsiku la Chitetezo mu m’nthawi inonso.
Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi abwera ngati malo opatulika mu M’nthawi ya Mzimu Woyera. Tiyenera kupereka chiyamiko kwa Iwo amene adatipulumutsa pakukhala nsembe zoperekera machimo aanthu onse. Tiyeneranso kugwiritsa ntchito chikondi chomwe talandira kuchokera kwa Mulungu kwa abale ndi alongo athu.
“Malo opatulika athu ndiwo mpando wachifumu wa ulemerero, wokhazikika pamsanje chiyambire. 13Inu Yehova, chiyembekezo cha Israele.”
Yeremiya 17:12–13
M’mawa mwake anaona Yesu alinkudza kwa iye, nanena, “Onani Mwanawankhosa wa Mulungu amene achotsa tchimo lake la dziko lapansi!”
Yohane 1:29
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi