Phwando la Malipenga ndi masiku khumi opemphera, omwe Mpingo wa Mulungu umasunga, ndi nthawi zowulula ndi kulapa machimo athu onse omwe tapanga chaka chatha. Choncho, anthu a Mulungu ayenera kukonzekera Tsiku la Chitetezero polapa kwathunthu kudzera mu pemphero.
Mzimu ukaleka kupemphera, komwe ndi kukupuma, mzimuwo umavutika kwambiri. Yesu, yemwe adabwera zaka 2,000 zapitazo, ndi Khristu Ahnsahnghong komanso Mulungu Amayi, omwe abwera mu M’nthawi ya Mzimu Woyera, adatiphunzitsa ife mphamvu ya pemphero ponena kuti, “Pemphani, funani, ndi kugogoda,” ndipo adapereka chitsanzo cha kuyenda mu njira ya uthenga wabwino ndi pemphero.
“ ‘Pemphani ndipo chidzapatsidwa kwa inu; funani, ndipo mudzapeza; gogodani ndipo chidzatsegulidwa kwa inu . . . kopambana kotani nanga Atate wanu wa Kumwamba adzapatsa zinthu zabwino kwa iwo akumpempha Iye!’ ”
Mateyu 7:7–11
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi