Tikamapemphera kwa Mulungu, kupempha
zinthu zakuthupi, ndipo Mulungu wayankha
mosiyana ndi zimene timayembekezera,
tinganene kuti, “Mulungu sayankha mapemphero anga.”
Komabe, si zoona.
Tiyenera kudziwa kuti ndi njira
ya chikondi cha Mulungu kutipatsa
ife madalitso a ufumu wakumwamba
umene umapindulitsa miyoyo yathu.
Chikondi cha mayi amene anadzipereka
yekha kuti apulumutse khanda pa tsiku
lozizira kwambiri la January 1951,
chimatipangitsa kuganizira za nsembe ya
Makolo athu auzimu, Khristu
Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Anadzipereka okha kuti achotse
machimo aanthu ndikupatsa anthu
ufumu wosatha wakumwamba.
Okondedwa, tikondane wina ndi mnzake:
chifukwa kuti chikondi chichokera kwa
Mulungu, ndipo yense amene akonda, abadwa
kuchokera kwa Mulungu, namzindikira Mulungu.
Iye wosakonda sazindikira Mulungu;
chifukwa Mulungu ndiye chikondi.
1 Yohane 4:7-8
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi