Maphwando oikika a Mulungu ndi mwayi
woperekedwa kwa ana a Mulungu okha!
Ngakhale pali mipingo yosawerengeka padziko lapansi
ndi mpingo wa Mulungu wokha, malo achifumu amene ali pakati pa miyamba,
umene Mulungu Mwini wake anakhazikitsa nakhumbapo pakhale pokhalapo pake;
apo Mulungu amadalitsa ndi chipulumutso ndi chikhululukiro cha machimo.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi