Zotsatira za moyo wathu wachikhulupiriro zimadalira ngati timadalira Mulungu kapena ayi. M’mbuyomu, pomwe A Israeli adagonjetsa Yeriko mchipululu, kugonjetsa adani 135,000, adakwanitsa kupambana ndi amuna ochepa chifukwa anali ndi chikhulupiriro chomawona chilichonse malinga ndi maonedwe a Mulungu.
David ndi Yoswa adayenda m’njira yachikhulupiriro, pokhala ndi malingaliro a Mulungu ndikukhulupirira nthawi zonse kuti Mulungu anali nawo ngakhale atakumana ndi zovuta zotani. Momwemonso, mamembala a Mpingo wa Mulungu amayenda njira yopambana ya uthenga wabwino ndikukhulupirira kuti Mulungu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi amakhala nawo nthawi zonse.
“koma wopanda chikhulupiriro sikutheka kumkondweretsa,pakuti iye wakudza kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti alipo ndi kuti ali wobwezera mphotho iwo akumfuna Iye.”
Ahebri 11:6
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi