Mulungu mmodzi Atate anachita udindo wa Atate ndi dzina la Yehova mu badwo wa Atate;
mu m’badwo wa Mwana, Iye anabwera ndi dzina la Yesu ndi kupereka chitsanzo kwa anthu monga Mwana;
mu m'badwo wa Mzimu Woyera, Iye anabwera kachiwiri ndi dzina la Khristu Ahnsahnghong.
Izi ndi zomwe Utatu umatanthauza.
Awo amene amamvetsetsa Utatu angakhulupirire ndi kuzindikira kuti zimene Mulungu Yehova anachita zinachitidwa ndi Yesu, ndipo zimene Yesu anachita zinachitidwa ndi Dzina Latsopano loti Khristu Ahnsahnghong.
Athanso kumvetsetsa kuti mu badwo wa Mzimu Woyera, Khristu Ahnsahnghong ayenera kubwera ndi Mulungu Amayi, Mkwatibwi wa Mzimu Woyera ndi kutsogolera anthu ku chipulumutso kudzera mu Paska wa pangano latsopano.
Ine, Inetu ndine Yehova; ndipo palibe Mpulumutsi, koma Ine ndekha.
Yesaya 43:11
Iye ndiye . . .
Ndipo palibe chipulumutso mwa wina yense, pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo la kumwamba, lopatsidwa mwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.
Machitidwe 4:11-12
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi