Tikayang’ana kuwalako, mthunzi umaonekera kumbuyo kwathu, koma tikatembenukira msana wathu ku kuwala, mthunzi umatchinga njira yathu.
Chimozimozi, pamene anthu apita kwa Mulungu amene ali kuunika, mdima sungathe kuwatsekereza.
Mofanana ndi Yeremiya m’nthaŵi ya Atate ndi atumwi a m’nthaŵi ya Mwana, pamene tipereka kuunika kwa ulemerero wa Mulungu, tingakumane ndi chizunzo ndi zopinga.
Komabe pamapeto pake tidzalandira madalitso ambiri.
Yesaya, Yeremiya, ndi Ezekieli anapereka kuunika kwa Mulungu Yehova m’nthaŵi ya Atate, ndipo mtumwi Paulo, Petro, ndi Yohane anapereka kuunika kwa ulemerero wa Yesu m’nthaŵi ya Mwana.
Momwemonso, mu nthawi ya Mzimu Woyera, mamembala a Mpingo wa Mulungu m’mayiko 175 padziko lonse lapansi amapereka kuwala kwa ulemerero wa Khristu Ahnsahnghong ndi Yerusalemu Amayi a Kumwamba omwe anabwera ngati Apulumutsi.
Pakuti taona, mdima udzaphimba dziko lapansi, ndi mdima wa bii mitundu ya anthu; koma Yehova adzakutulukira ndi ulemerero wake udzaoneka pa iwe. Nations will come to your light, and kings to the brightness of your dawn.” Ndipo amitundu adzafika kwa kuunika kwako, ndi mafumu kwa kuyera kwa kutuluka kwako.
Yesaya 60:1-3
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi