Yesu Khristu anatiphunzitsa njira yolandirira madalitso ambiri, njira yolandila chikhululukiro cha machimo, ndi njira yolowera mu Ufumu wa Kumwamba. Komabe, Yesu anali ndi nkhawa komanso kukhumudwa ndi Ayuda omwe amamuneneza ndipo adachita tchimo lalikulu lofuna kumuponya miyala.
Khristu Ahnsahnghong ndi Amayi Akumwamba Yerusalemu Watsopano adabwezeretsa chowonadi cha Pangano Latsopano lomwe lidathetsedwa kuyambira AD 325, ndipo adatipatsa madalitso a chikhululukiro cha machimo ndikuwononga imfa kwamuyaya kudzera mu mkate ndi vinyo wa Pasika. Anthu omwe amazindikira Mzimu ndi Mkwatibwi ndikuwatsata ali odalitsika.
Iye ananena kwa iwo, “Koma inu mutani kuti Ine ndine yani?” Ndipo Simoni Petro anayankha nati, “Inu ndinu Khristu, Mwana wa Mulungu wamoyo.” Ndipo Yesu anayankha iye nati, “Ndiwe wodala, Simoni Bara-Yona . . . Ndidzakupatsa mafungulo a Ufumu wa Kumwamba . . .”
Mateyu 16:15–19
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi