Owonerera amene alibe chidwi mu uthenga wabwino sangalandire cholowa cha ufumu wa kumwamba. Chifukwa chake, tiyenera kutenga nawo mbali mwaudindo mu ntchito ya chipulumutso, imene ikutsogoleredwa ndi Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai, tili ndi Malingaliro a Umwini, monga momwe anachitira Mtumwi Paulo.
Monga mwambi umati, “Iye amene ali ndi udindo ndiye mwini, ndipo iye amene alibe udindo ndiye mlendo,” anthu a Mulungu amene aitanidwa kukhala antchito a pangano latsopano ayenera kulalikira ku dziko lonse Choonadi cha pangano latsopano, chimene chingatsogolere anthu ku chipulumutso.
Ndipo anadza nalankhulanso nati, “. . . Chifukwa chake mukani, phunzitsani anthu a mitundu yonse, ndi kuwabatiza iwo m'dzina la Atate, ndi la Mwana, ndi la Mzimu Woyera, ndikuwaphunzitsa asunge zinthhu zonse zimene ndakulamulirani inu. . . .” Mateyu 28:18–20
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi