Ndani Amatikhululukira Machimo Athu Kudzera mu Paska wa Pangano Latsopano? Kupulumutsa anthu amene anabwera padziko lapansi, atachita machimo oyenera imfa mu ufumu wakumwamba, Mulungu mwini anabwera padziko lapansi mu thupi ndi dzina la Yesu mu m'badwo wa Mwana, ndi dzina la Ahnsahnghong mu m' badwo wa Mzimu Woyera pamodzi ndi Amai a Kumwamba.
Mpingo wa Mulungu Umasunga Paska Padziko Lonse Lapansi Ndi Khristu Ahnsahnghong yekha amene anakonza phwando la kumeza imfa kudzera mu Paska wa pangano latsopano amene anali asakusungidwa kwa nthawi yaitali kuyambira kuthetsedwa kwake mu AD 325.
Ndipo m'phiri limeneli Yehova wa makamu adzakonzera anthu ake onse phwando la zinthu zonona, phwando la vinyo wa pamitsokwe, la zinthu zonona za mafuta okhaokha, la vinyo wansenga wokuntha bwino. Yesaya 25:6–8
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi