Monga momwe mbiri ya Chipangano Chakale ikuwonetsera, Aisraeli auzimu ayenera kulandira Khristu Ahnsahnghong yemwe wabweretsa Paskha Pangano Latsopano, Urimu ndi Tumimu,
kuti amasulidwe ku Babulo ndikulandiridwa kuti ndi “anthu enieni a Mulungu.”
Lero, mamembala a Mpingo wa Mulungu amadya ndikumwa thupi ndi mwazi wa Yesu, yemwe ndi kachisi, kudzera mu mkate ndi vinyo wa Paskha wa Pangano Latsopano.
Zikutanthauza kuti ali ndi mwayi wokhala ansembe okudya chakudya chopatulika kwambiri chomwe chimachokera kumalo opatulikawo.
Awa anafunafuna maina ao m’buku la iwo owerengedwa mwa chibadwidwe chao, koma osawapeza; potero anachotsedwa ku ntchito ya nsembe monga odetsedwa. . . . kuti asadyeko zopatulika kwambiri, mpaka adzabuka wansembe wokhala ndi Urimu ndi Tumimu. Ezra 2:62–63
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi