Chifukwa chimene Mulungu analengera zamoyo zonse padziko lapansi pano kuti zilandire moyo kudzera mwa mayi chinali kutidziwitsa kuti moyo wosatha umaperekedwa kudzera mwa Amayi athu auzimu okha basi.
Chifukwa chimene Mulungu anatiphunzitsira ife kuti Iye ndi “Atate,” ndipo ife ndife ana ake aamuna ndi aakazi akafuna kuwulula Mulungu Amayi kupyolera mu maudindo a aliyense m’banjamo.
Anthu amaona kuti n’kofunika kukonzekera zopuma pantchito pamene amakukhala ndi moyo waufupi padziko lino lapansi. Koma kunena zoona, n’kofunika kwambiri kupanga mapulani ndi kukonzekera dziko la angelo limene tidzakhalako kosatha.
Iwo amene akuyembekezadi ufumu wakumwamba akulandira Atate Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi amene abwera ngati Apulumutsi mu m'badwo wa Mzimu Woyera. Iwo amasunganso tsiku la Sabata ndi Paskha wa pangano latsopano monga ana a banja lakumwamba.
Muyenera inu, Ambuye wathu, ndi Mulungu wathu, kulandira ulemerero ndi ulemu ndi mphamvu; chifukwa mudalenga zonse, ndipo mwa chifuniro chanu zinakhala, ndipo zinalengedwa.
Chivumbulutso 4:11
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi