Chifukwa chimene ntchentche zimakhalira tsiku limodzi, agalu amakhala zaka 15, ndipo anthu amakhala zaka 100 ndi chifukwa chakuti anatengera utali wa moyo umenewo kuchokera kwa amayi awo. Anthu onse angakhale “ana a lonjezano” amene amalandira moyo wosatha kwa Mulungu pokhapo pamene tikumana ndi Mulungu Amayi amene ali ndi moyo wosatha.
Baibulo limatiphunzitsa za banja lakumwamba kupyolera mu dongosolo la banja la padziko lapansi limene lili mthunzi, ndi za Atate ndi Amayi akumwamba kupyolera mwa Adamu ndi Hava ndi Mwanawankhosa ndi Mkazi Wake (Mkwatibwi). Baibulo limaphunzitsanso kuti Mulungu Amayi yekha, amene ali ngati Yerusalemu, ali ndi moyo wosatha.
Ndipo icli lonjezo limenen anatilonjeza ndiwo moyo wosatha.
1 Yohane 2:25
po ananditenga mu Mzimu kunka kuphiri lalikulu ndi lalitali, nandionetsa mzinda wopatulikawo, Yerusalemu, wotsika m’Mwamba kuchokera kwa Mulungu,
Chivumbulutso 21:10
Koma Yerusalemu wa kumwamba uli waufulu, ndiwo amai wathu. . . . Koma ife, abale, monga Isaki, tili ana a lonjezano.
Agalatiya 4:26–28
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi