Paska si chikondwerero chokhalira kudya mkate ndi kumwa chikho cha vinyo. Ndi tsiku lolandila lonjezo la chipulumutso polandira chisindikizo ngati anthu a Mulungu komanso ndi chikondwerero cha chiyembekezo, chomwe chimapereka moyo wosatha kwa anthu omwe moyo wawo ndi wakanthawi.
Mulungu anabwera ndi kugonjetsa mphamvu za Satana ndi kupereka moyo wosatha kwa ana a Mulungu.
Mu M’badwo wa Mwana anali Yesu yekha, ndi mu M’badwo wa Mzimu Woyera ndi Khristu yekha Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi amene amapatsa anthu Paska wa Pangano Latsopano amene ali ndi lonjezo la moyo wosatha.
Ndipo m'phiri limeneli Yehova wa makamu adzakonzera anthu ake onse phwando la zinthu zonona, phwando la vinyo wa pamitsokwe. . .Iye wameza imfa kunthawi yonse. . . .Ndipo adzanena tsiku limenelo, Taonani, uyu ndiye Mulungu wathu; tamlindirira Iye, adzatipulumutsa; Yesaya 25:6–9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi