“Mgonero Womaliza” ndi ntchito ya luso lodziwika bwino kwa anthu padziko lonse lapansi. Yesu anali wofunitsitsa kuchita Paska wa Pangano Latsopano. Kudzera mu choonadi ichi, titha kutsogozedwa ndi Mulungu molondola kuyenda munjira yotsogolera yakumwamba.
Paska ndi phwando lomwe Yosiya, Hezekiya, ndi Yoswa onse adayamikiridwa pokondwerera. Phwando la moyo ili lidawabweretsera madalitso ambiri komanso kupambana pankhondo.
Mu M’badwo wa Mzimu Woyera, anthu atha kulandira moyo ndi lonjezo lakumwamba pokondwerera Paska molingana ndi chitsanzo cha Khritsu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi ,.
“ ‘Pakuti ndakupatsani inu chitsanzo, kuti, monga Ine ndakuchitirani inu, inunso muchite.’ ” Yohane 13:15
“Ndipo anati kwa iwo, ‘Ndinalakalaka ndithu kudya Paska uwu pamodzi ndinu, ndisanayambe kusautsidwa’ ” Luka 22:15
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi