M’moyo wathu, pali zinthu zambiri
zosiyanasiyana, monga kuchita ntchito
zosiyanasiyana komanso kukulitsa chidziwitso.
Komabe, pamapeto pake, pokhapo pamene tipeza
Mzimu ndi Mkwatibwi, Atate Ahnsahnghong ndi
Mulungu Amayi, tingathe kulandira madzi a moyo,
kukhululukidwa machimo athu, ndi kubwerera
ku nyumba yathu yamuyaya, ufumu wakumwamba.
Baibulo, lomwe ndi bukhu la maulosi olembedwa ndi
iwo amene anatsogozedwa ndi Mzimu Woyera, linaneneratu
kuti Mulungu, Kuwala kwa Choonadi, adzabwera pa
dziko lapansi mumdima ndi kupulumutsa anthu ndi kuti
Satana m’munda wa Edeni, amene amatsutsa Mulungu
Amayi, adzakumana ndi chiwonongeko.
[N]dipo ndidzaika udani pakati pa iwe ndi
mkaziyo, ndi pakati pa mbeu yako ndi
mbeu yake; ndipo idzalalira mutu wako,
ndipo iwe udzalalira chitendeni chake.
Genesis 3:15
Ndipo chinjoka chinakwiya ndi mkazi, ndipo
chinachoka kunka kuchita nkhondo ndi otsala
a mbeu yake, amene asunga malamulo a Mulungu,
nakhala nao umboni wa Yesu. Ndipo chinjokacho
chinakaimirira m'mbali mwa nyanja.
Ndipo ndinaimirira pa mchenga wa nyanja. . . .
Chivumbulutso 12:17–13:1
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi