Miyambo yachipembedzo ya Mpingo wa Katolika ndi mipingo ina okhala ndi mazira owiritsa ndi akalulu sizinachokere m’Baibulo. Zinachokera ku kulambira mulungu wamkazi Isitala. Ngati anthu a Mulungu atenga nawo pa kulambira Isitala, masoka adzawagwera.
Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu limasunga Tsiku la Kuuka kwa Akufa molingana ndi Baibulo ponyema mkate monga momwe Yesu ndi ophunzira ake adachitira zaka 2,000 zapitazo.
Ndipo kunali m'mene Iye anaseama nao pachakudya, anatenga mkate, naudalitsa, naunyema, napatsa iwo. Ndipo maso ao anatseguka, ndipo anamzindikira Iye; ndipo anawakanganukira Iye, nawachokera. Luka 24:30-31
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi