Mulungu amaona mathero kuyambira pachiyambi ndipo amatsogolera anthu ku njira ya chipulumutso. Monga Yoswa ndi Kalebe anapulumutsidwa pakumvera Mulungu, amene amaona m’tsogolo, ndi chikhulupiriro m’mawu ake, leronso, Mulungu akupulumutsa iwo omvera mawu Ake, osati maganizo awo.
Yesu anagwira ntchito ya chipulumutso, kulosera kuti Petro adzamukana Iye katatu komanso kuti Yudasi Isikarioti adzamupereka. Momwemonso, Khristu Ahnsahnghong analengezelatu kuti adzakwera Kumwamba akamaliza ntchito Yake, ndipo anatiphunzitsa kuti tiyenera kutsatira Mulungu Amayi pa chipulumutso chathu.
“Ndilalikira za chimaliziro kuyambira pachiyambi, ndi kuyambira nthawi zakale ndinena zinthu zimene zisanachitidwe; ndi kunena, Uphungu wanga udzakhala, ndipo ndidzachita zofuna zanga zonse.”
Yesaya 46:11
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi