Amene samvera sangalowe mu ufumu wa kumwamba, womwe ndi dziko la Kanani, monga momwe tikuonera m’mbiri ya Chipangano Chakale.
Kudzera m’mbiri imeneyi, titha kuona mmene Mfumu Zedekiya anali womvera poyamba koma pambuyo pake anatembenukira ku kusamvera, ndi mmene Mfumu Sauli analiri theka womvera ndi theka wosamvera, pamodzi ndi anthu amene sanamvere kuyambira pachiyambi. Anthu amenewa sangapulumuke, koma amene amatsatira Mwanawankhosa kulikonse kumene akupita ndi kumvera adzapulumuka.
Khristu Ahnsahnghong, amene anabwera ngati Mwanawankhosa, anatsimikizira kudzera m’Baibulo kuti amene amamvera mawu a Mulungu adzapita kumwamba. Iye anasiyira anthu ziphunzitso Zake, nati, “Mukamvera ndi mtima wonse ziphunzitso za Mulungu Amayi, zinthu zabwino zambiri zimene simunayembekezere zidzachitika.
Muzisamalira kuchita malamulo onse amene ndikuuzani lero lino, kuti mukhale ndi moyo, ndi kuchuluka, ndi kulowa, ndi kulandira dziko limene Yehova analumbirira makolo anu.... kuti akuchepetseni, kukuyesani, kudziwa chokhala mumtima mwanu, ngati mudzasunga malamulo ake, kapena iai.
Deuteronomo 8:1-2
Ndipo adawalumbirira ayani kuti asalowe mpumulo wake? Si awo kodi osamverawo? Ndipo tiona kuti sanathe kulowa chifukwa cha kusakhulupirira.
Ahebri 3:18-19
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi