Monga momwe anthu omwe atayika panyanja yayikulu kapena m’phiri amafunikira kampasi, chinthu chomwe chimagwira ngati kampasi ya anthu omwe atayika panjira yopita Kumwamba ndi mawu a Mulungu olembedwa m’mabuku 66 a m’Baibulo.
Monga atumwi omwe amakhulupirira kuti nzeru ya chipulumutso ndi chuma yabisika mwa Yesu, mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhulupirira kuti njira ya chipulumutso ndi njira yopita Kumwamba zili mwa Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi amene abwera monga Mzimu ndi Mkwatibwi. Mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhala, akumvera mawu a Mulungu.
Mawu anu ndiwo nyali ya ku mapazi anga, ndi kuunika kwa panjira panga.
Masalmo 119:105
Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi anena, “Idzani!” Ndipo wakumva anene, “Idzani!” Ndipo wakumva ludzu, adze; iye wofuna atenge madzi a moyo kwaulere.
Chiv 22:17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi