Satana poyamba anawononga tsiku la Sabata, lamulo la Mulungu, lomwe ndi njira ya chipulumutso.
Pambuyo pake, pamene malamulo onse a Mulungu adasowa, dziko lapansi lidadzazidwa ndi kusaweruzika,
ndipo njira ya chipulumutso idatsekedwa monga phunzitso lokuswa zenera.
Aliyense adzakumana ndi chiweruzo cha Mulungu chomwe chidzasankhe ngati atapite Kumwamba kapena ku gehena.
Mu M’badwo wa Mzimu Woyera, chisomo chopita Kumwamba chaperekedwa kwa iwo omwe amasunga malamulo a Mulungu, pangano latsopano, chomwe Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi abweretsanso.
‘‘Mverani Ine ndi kuchita chilichonse chimene ndakulamulirani. Mukatero mudzakhala anthu anga ndi Ine ndidzakhala Mulungu wanu.’ ‘‘ Yeremiya 11:4
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi