Tsiku la Sabata ndilo chikumbutso cha Alengi, chomwe chimatilola ife kuopa Mulungu Alengi ndi kuzindikira mphamvu Zawo ndikulola anthu kubwerera kwa Mulungu. Ndi chizindikironso kwa ana a Mulungu. Ichi ndi chifukwa chake Satana anasintha tsiku la Sabata kukhala mapemphero a Lamulungu kuti anthu asabwere kwa Mulungu.
Zinalembedwa m’Baibulo kuti Solomo anali pambali pa Mulungu ndipo anamva mawu a Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi pamene Mulungu ananena pachiyambi kuti, “Tipange munthu m’chifanizo Chathu.” Momwemonso, mamembala a Mpingo wa Mulungu azindikira Mulungu Elohimu kupyolera mu ziphunzitso za Baibulo ndi aneneri, ndi kuopa Mulungu, ndi kusunga malamulo a Mulungu monga mwalembedwa m’mawu anzeru.
Chifukwa chake ndikonda malamulo anu
koposa golide, inde golide woyengeka.
Chifukwa chake ndiyesa ngolunjika
malangizo anu onse akunena zonse;
koma ndidana nazo njira zonse zonyenga
Masalimo 119:127-128
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi