Popeza anthu sangaone dziko lauzimu chifukwa chakuti ali m’thupi, amakonda kufunafuna Mulungu kuti athetse mavuto amene amakumana nawo m’moyo wawo. Komabe, tsopano tiyenera kusunga malamulo a Mulungu kudzera mwa amene Mulungu analonjeza kuti adzabwezeretsa chikhalidwe chathu choyambirira ndi kutitsogolera ku Ufumu wakumwamba waulemerero ndi wosatha.
Mpingo wa Mulungu ndi mpingo woona umene unamangidwa pa maziko a atumwi ndi aneneri. Mamembalawa akupemphera m’dzina la Khristu Ahnsahnghong amene anabwera ndi dzina latsopano la Yesu mu M’badwo wa Mzimu Woyera, ndipo amakhulupirira mwa Yerusalemu Mulungu Amayi amene Khristu Ahnsahnghong anawachitira umboni.
Iye wakupambana, ndidzamyesa iye mzati wa m’Kachisi wa Mulungu wanga . . . ndi dzina la mzinda wa Mulungu wanga, la Yerusalemu watsopano . . . ndi dzina langa latsopano.
Chivumbulutso 3:12
Pamenepo ndipo simulinso alendo ndi ogonera, komatu muli a mudzi womwewo wa oyera mtima ndi a banja la Mulungu; Omangika pa maziko a atumwi ndi aneneri . . .
Aefeso 2:19–20
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi