Monga momwe chilichonse chilili ndi nthawi yake, ndi nyengo yake pa chilichonse, moyo wathu wachikhulupiriro ulinso ndi cholinga chomveka bwino: chipulumutso cha miyoyo yathu—ndiko kuti, kulandira moyo wosatha.
Kuti atipulumutse, Mulungu anachita ntchito Yake yowombola anthu kwa zaka zoposa 6,000, naigawa m'mibadwo itatu— m'mibadwo wa Atate, m'mibadwo wa Mwana, ndi m'mibadwo wa Mzimu Woyera—ndipo anatipatsa dzina losiyana la Mpulumutsi mu m'mibadwo uliyonse.
Mu nthawi ya Atate, dzina la Mpulumutsi linali Yehova. Pamene nthawi inasintha kufika pa nthawi ya Mwana, anali Yesu. Komabe, tsopano tikukhala mu nthawi ya Mzimu Woyera. Choncho, chipulumutso sichingalandiridwe kudzera m'dzina la Yehova kapena la Yesu. Pokhapokha tikadziwa dzina latsopano la Yesu ndikuitana pa dzina limenelo, tingapulumuke.
Dzina latsopano la Yesu—dzina limene limapereka dalitso la moyo wosatha kwaulere mu m’badwo wa Mzimu Woyera—ndi Khristu Ahnsahnghong.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi