Mulungu Wamphamvuyonse, amene analenga kuwala ndi kulenga zinthu zonse ndi mawu ake, anabwera padziko lapansi pano kachiwiri.
Mu 1948 pamene nthambi za mtengo wa mkuyu [Israeli], zimene zinafota kwa zaka 1,900, zinakhala zanthete ndipo masamba ake anaphukira, Khristu anadza ku Korea, nayamba kulalikira uthenga wabwino.
Dziko, lomwe aneneri a Israeli adalosera kuti ndi malo omwe Khristu adzabweranso, linali kumalekezero a dziko lapansi kummawa-Korea.
Khristu anasankha kuvutika chifukwa cha chipulumutso chathu.
Komabe, tinangofuna mkate wa thupi lathu, osati mkate wa moyo wa mizimu yathu.
“Yesu anatipatsa pangano la moyo: Ngati mudya thupi langa ndi kumwa mwazi wanga, muli nawo moyo mwa inu. Palibe chozizwitsa choposa ichi.”
Mkate wa moyo ndi thupi ndi mwazi wa Khristu.
“Tengani, idyani; mkate wa Paskha ndiwo thupi langa.”Mt 26:26
“Pakuti ichi ndi mwazi wanga wa pangano wothiridwa chifukwa cha anthu ambiri ku kuchotsa machimo.“Mat 26:27-28
Khristu anayenera kubwera kachiwiri ndi Paskha wa Pangano Latsopano kuti atipulumutse.
Khristu asanabwerere Kumwamba, anangofuna chinthu chimodzi:
Ndichakuti inu mulandire chipulumutso.
Khristu akanapanda kubwera pa dziko lapansi, sitikadadziwa kuti chikondi n’chiyani.
Khristu akanapanda kuvutika, sitikadadziwa kuti nsembe ndi chiyani.
Ngati Khristu akadakhala Kumwamba kokha, sitikanamulakalaka Iye.
Timakonda Khristu amene anabwera kachiwiri kudzatipulumutsa.
Mwamva? Kodi mukumva Khristu akugogoda pa khomo la mtima wanu?
Khristu amakukondani. Iye akufuna kukupatsani inu moyo wosatha.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi