Ngakhale kuti zinatsimikiziridwa m’Baibulo lonse, anthu ena amalephera kukhulupirira Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi, ndipo ngakhale amaitana Mulungu kuti “Atate,” sasunga Paska wa pangano latsopano, yemwe ndi njira yolandirira thupi ndi mwazi wa Mulungu.
Anthu oterewa adzatha kulekana ndi Mulungu.
Mulungu anati, “Ine ndidzakhala Atate kwa inu, ndipo inu mudzakhala ana Anga,” ndipo kudzera maudindo awa a m’banja, Iye anatiwunikira kuti anthu ndi banja lauzimu kumwamba.
Chifukwa chake, mamembala a Mpingo wa Mulungu, monga banja lakumwamba, amakhulupirira Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi, ndikuyenda njira ya chikhulupiriro, kukondana wina ndi mzake monga abale ndi alongo.
Chifukwa chake, . . . ndipo Ine ndidzalandira inu,
ndipo ndidzakhala kwa inu Atate, ndi inu mudzakhala kwa Ine ana aamuna ndi aakazi, anena Ambuye Wamphamvuyonse.
2 Akorinto 6:17–18
Koma Yerusalemu wa kumwamba uli waufulu, ndiwo amai wathu.
Agalatiya 4:26
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi