Kuti atsogolere ana ake ku dziko la angelo kumene kulibe imfa, Mulungu anabwera ku dziko lapansi ndipo anadutsa m’masautso onse ngakhale imfa imene anthu amakumana nayo m’thupi, kusonyeza chikondi Chake chopanda malire pa ana Ake.
Ndi Khristu Ahnsahnghong yekha ndi Mulungu Amayi amene atilola ife njira ya kumoyo wosatha kudzera mu mkate ndi vinyo wa Paskha molingana ndi ulosi wa m’Baibulo wakuti Mulungu wathu amatipatsa moyo wosatha mu Ziyoni. Choncho, Mpingo wa Mulungu umakhulupirira kuti Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi ndi Apulumutsi.
Koma timpenya Iye, amene adamchepsa pang’ono ndi angelo ndiye Yesu, chifukwa cha zowawa za imfa, wovala korona wa ulemerero ndi ulemu kuti ndi chisomo cha Mulungu alawe imfa m’malo mwa munthu aliyense.
Ahebri 2:9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi