Monga aliyense ali ndi atate ndi amayi omwe adawabereka mwakuthupi, pali Atate wauzimu ndi Amayi auzimu omwe amatipatsa moyo wosatha m'dziko la angelo.
Pokhulupirira zimenezi, tiyenera kusunga Paska wa pangano latsopano, njira yokhayo yokhalira ana a Mulungu.
Ana a Mulungu, omwe adzalamulire mu ufumu wakumwamba kwamuyaya, ayenera kudziwa dzina la Mulungu.
Monga oyera analandira dzina la Yesu ndipo anapulumutsidwa mu m'badwo wa Mwana, mamembala a Mpingo wa Mulungu alandire Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi mu m'badwo wa Mzimu Woyera, kulalikira dzina la Mulungu ku dziko lonse lapansi ndi kupereka uthenga wa chipulumutso.
Koma ngati mukhala opanda chilango, chimene onse
adalawako, pamenepo muli am'thengo, si ana ai.
Komanso, tinali nao atate a thupi lathu akutilanga, ndipo tinawalemekeza;
kodi sitidzagonjera Atate wa mizimu koposa nanga, ndi kukhala ndi moyo?
Ahebri 12:8–9
Ena atama magaleta, ndi ena akavalo; koma ife
tidzatchula dzina la Yehova Mulungu wathu.
Masalimo 20:7
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi