Monga momwe kuli banja lenileni padziko lapansi
pano, kumwambanso kuli banja la kumwamba.
Thupi la Mulungu ndi mwanzi wake zinalonjezedwa
pa Paskha wa pangano latsopano.
Kudzera mu Paskha uyu, mamembala a Mpingo wa Mulungu amasanduka kukhala ana aamuna ndi aakazi a Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi, ndipo anasandika kukhala a m’banja la kumwamba.
Ziŵalo zenizeni za banja lakumwamba zimasamalirana ndi
kugwirizana wina ndi mnzake kuti pasakhale
wozimva wosalidwa.
Komanso, akuyenda panjira yopita ku ufumu wakumwamba
pamodzi, pa kulimbikitsidwa ndi mawu a Mulungu.
Amene atumikira chifaniziro ndi mthunzi wa zakumwambazo . . .
Ahebri 8:5
Mbado wa luso la makono (AI) ukuyandikira.
Komabe, Mulungu sanaikire uthenga wabwino ku luso
lamakonoli kuti lipereke madalitso kwa ana ake.
Mulungu anaunikira ana ake kuti apeze achibale
otayika akumwamba mwamsanga ndi kulowa mu ufumu
wa ulemerero wa kumwamba pamodzi.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi