Baibulo limatiphunzitsa kuti amene
amasunga malamulo a Mulungu
ndi amene angasangalatse Mulungu
pa kuyenda ndi Iye.
Ndiwo amene potsirizira pake
adzakwera kumwamba.
Monga makolo achikhulupiriro ngati
Enoki, Eliya, ndi Petro,
amene anakondweretsa Mulungu, mamembala
a Mpingo wa Mulungu
amakondweretsa Mulungu mwa kusunga
malamulo a Mulungu.
Ndiwo amene akuyenda ndi
Mzimu Woyera—Mulungu Ahnsahnghong,
ndi Mulungu Amayi amene
ndi zenizeni za pangano latsopano.
kwa iwonso anadzionetsera yekha
wamoyo ndi zitsimikizo zambiri,
zitatha zowawa zake, naonekera
kwa iwo masiku makumi
anai, ndi kunena zinthu
za Ufumu wa Mulungu; . . .
Ndipo m'mene adanena izi,
ali chipenyerere iwo, ananyamulidwa;
ndipo mtambo unamlandira Iye
kumchotsa kumaso kwao.
Machitidwe 1:3-9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi