M’nthawi ya Babulo,
pamene Danieli analipo,
Mulungu analosela za
maufumu amene adzauka
m’tsogolo, monga Mediya
ndi Perisiya, Griki, ndi Roma.
Ndiponso, Mulungu anachitira
umboni kuti Baibulo limaposa sayansi.
Kupyolera mu zinthu
zimenezi, Mulungu anafuna
kuti anthu akhulupirire
ndi kukhala ndi chiyembekezo
cha ufumu waulemerero
wakumwamba kumene adzalowe m’tsogolo.
Zinthu zonse zinakwaniritsidwa
molingana ndi maulosi
a m’Baibulo—moyo
wa Khristu Wobwera
Koyamba, maulosi onena
za Kudza Kwachiwiri
kwa Khristu Ahnsahnghong
ndi Mulungu Amayi,
ndi ufulu wa Israeli mu 1948.
Palinso maulosi amene
Mulungu anasiyira anthu,
omwe ali pangozi chifukwa
cha zionongeko zosiyanasiyana
ndi mavuto a nyengo.
Mulungu ananena kuti
anthu ayenera kulowa
mwamsanga ku Ziyoni,
kumene angapulumuke Kuzionongeko.
[M]wa izi dziko lapansi
la masiku aja, pomizika
ndi madzi, lidaonongeka;
koma miyamba ndi
dziko la masiku ano,
ndi mau omwewo zaikika
kumoto, zosungika kufikira
tsiku la chiweruzo ndi
chionongeko cha anthu osapembedza.
2 Petulo 3:6-7
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi