Monga momwe Mulungu anaperekera chingalawa monga
pothawirapo m’nthawi ya Nowa asanawononge dziko lapansi
ndi madzi, Mulungu, amene wabwera monga Davide wauzimu,
anakhazikitsa Ziyoni wauzimu kumene mapwando a Mulungu
amachitidwa ndi kulangiza anthu kuthawira ku Ziyoni
asanaweruze dziko ndi moto pa tsiku lomaliza.
Yesu atakwera kumwamba, mdierekezi anayesa
kuwononga Ziyoni pothetsa maphwando a Mulungu,
koma monga kunaloseredwa, Khristu Ahnsahnghong
anabwezeretsanso maphwando asanu
ndi awiriwo katatu ndi tsiku la Sabata.
Choncho, Mpingo wa Mulungu nthawi
zonse umadzazidwa ndi phokoso
lachisangalalo ndi kukondwa ndi
chiyembekezo cha chipulumutso.
Pakuti Yehova watonthoza mtima wa Ziyoni , watonthoza
mtima wa malo ake onse abwinja; ndipo wasandutsa chipululu
chake ngati Edeni, ndi malo ake ouma ngati munda wa
Yehova; kukondwa ndi kusangalala kudzapezedwa
m’menemo, mayamikiro, ndi mau a nyimbo yokoma.
Yesaya 51:3
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi