Mu nthawi ya Mpingo woyambirira pamene Mulungu amene Ayuda onse ankakhulupirira mwa iye anabwera mu thupi ndi dzina la Yesu, iwo sanamuzindikire Iye koma anamupachika Iye.
Chimodzimodzinso masiku ano, anthu ambiri achipembedzo amalephera kuzindikira kuti Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu amene anabweranso kudzapulumutsa anthu. Iwo akumukana Iye, kutengeka kuchoka ku njira ya chipulumutso.
Kudza Kwachiwiri kwa Khristu Ahnsahnghong analenga chilengedwe chonse, anapereka moyo kwa anthu, ndipo anatiphunzitsa za ufumu wosatha wakumwamba.
Iye ndi Mulungu amene anaonekera kuchokera ku South Korea, dziko lakutali la kum’maŵa, monga kunaloseredwa mu Chivumbulutso 7.
Anagwira ntchito ya chipulumutso mu Mpingo wa Mulungu kudzera mu Paska wa pangano latsopano (chidindo cha Mulungu).
Ndipo Yesu, pamene anadza ku dziko la ku Kesareya-Filipi, anafunsa ophunzira ake, kuti, . . .
Koma inu munena kuti ndine yani?
Ndipo Simoni Petro anayankha nati, Inu ndinu Khristu , Mwana wa Mulungu wamoyo.
Mateyu 16:13-16
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi