Kudzera mu mbiri yakale yomwe Yesu anakwera kumwamba zaka 2,000 zapitazo, Mulungu watipatsa chiyembekezo chokwera kumwamba–chiyembekezo cha moyo kuti tidzasandulika ndi mphamvu ya Mulungu ndikakumana ndi Ambuye mu mlengalenga.
Enoch nthawi zones ankayenda ndi Mulungu, ndipo anakwera wamoyo Kumwamba, pokhala ovomereza ngati modzi amene anakondweretsa Mulungu. Nowa nayonso akayenda ndi Mulungu nthawi zonse, ndipo anapulumutsidwa ku chiweruzo cha madzi. Elisha anatsatira Eliya kufikira kumamalidzilo mpaka tsiku limene Eliya anakwera Kumwamba, ndipo analowa m'malo mwake ngati mneneri.
Lero, mamembala a Mpingo wa Mulungu akukhala moyo wolapa zimene zimakondweretsa Mulungu,pa kuyenda ndi Atate Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi pa njira ya uthenga wabwino ndi chiyembekezo cha kukwera kumbamba.
Ndi chikhulupiriro Enoki anatengedwa kuti angaone imfa . . . anachitidwa umboni kuti anakondweretsa Mulungu; Ahebri 11:5
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi