Ngakhale titayang'ana makalendala, madikishonale, mabuku a Katolika, ndi Baibulo, tingaone kuti tsiku la Sabata, tsiku lolambirira lomwe Mulungu analisankha, ndi Loweruka.
Yesu ndi ophunzira ake ankasunga tsiku la Sabata, osati kulambira pa Sunday.
Anthu a Mulungu ayenera kusunga tsiku la Sabata [Loweruka] limene Mulungu adalikhazikitsa.
Gulu Lautumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu limalambira pa Sabata la tsiku lachisanu ndi chiwiri [Loweruka] loikidwa ndi Mulungu.
Ndipo anadza ku Nazarete, kumene analeredwa; ndipo tsiku la Sabata analowa m'sunagoge, monga anazolowera, naimiriramo kuwerenga m'kalata. Luka 4:16
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi