Pamene Nowa anamanga chingalawa,
pamene Mose anagaŵa Nyanja
Yofiira, pamene Gidiyoni anamenyana
ndi Midyani, ndipo pamene Yosefe
anakhala kazembe wa Ejipito, onse anavutika.
Komabe, chitsogozo chodabwitsa
cha Mulungu chinabisidwa
mmenemo kuti apereke madalitso
aakulu kwa amene
amamvera mawu a Mulungu.
Mu m’badwo uno, Mzimu Woyera
Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu
Amayi, Mkwatibwi, abwera ku dziko
lino lapansi, ndipo mamembala a Mpingo
wa Mulungu amene atsogozedwa ku Ziyoni
akupita kukalalikira uthenga wabwino padziko lonse lapansi;
zonsezi ndi zochita za Mulungu
za chipulumutso cha anthu
mu nthawi ya Mzimu Woyera.
Tsopano musapwetekwe mtima,
musadzikwiyira inu nokha, kuti
munandigulitsa ine kuno, . . .
Ndipo Mulungu anatumiza ine
patsogolo panu kuti ndikhazike
inu otsala m’dziko lapansi, ndi
kusunga inu amoyo ndi
chipulumutso chachikulu.
Ndipo tsopano sindinu amene
munanditumiza ine ndifike
kuno, koma Mulungu, . . .
Genesis 45:5-8
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi